Salimo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+N’chifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?+N’chifukwa chiyani simukumva mawu a kubuula kwanga?+ Yesaya 53:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma zinamukomera Yehova kuti mtumiki wake aphwanyidwe.+ Iye anamulola kuti adwale.+ Mukapereka moyo wake monga nsembe ya kupalamula,+ iye adzaona ana ake.+ Adzatalikitsa masiku ake+ ndipo ndi dzanja lake, adzakwaniritsa zokonda+ Yehova.+ Maliko 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo cha m’ma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” Mawu amenewa akawamasulira amatanthauza kuti: “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+
22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+N’chifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?+N’chifukwa chiyani simukumva mawu a kubuula kwanga?+
10 Koma zinamukomera Yehova kuti mtumiki wake aphwanyidwe.+ Iye anamulola kuti adwale.+ Mukapereka moyo wake monga nsembe ya kupalamula,+ iye adzaona ana ake.+ Adzatalikitsa masiku ake+ ndipo ndi dzanja lake, adzakwaniritsa zokonda+ Yehova.+
34 Ndipo cha m’ma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” Mawu amenewa akawamasulira amatanthauza kuti: “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+