Yohane 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anati: “Chakudya+ changa ndicho kuchita chifuniro+ cha amene anandituma ndi kutsiriza ntchito yake.+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
34 Yesu anati: “Chakudya+ changa ndicho kuchita chifuniro+ cha amene anandituma ndi kutsiriza ntchito yake.+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+