Salimo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Agalu andizungulira.+Khamu la anthu ochita zoipa landizinga.+Iwo akuluma manja ndi mapazi anga ngati mkango.+ Salimo 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ine chikhulupiriro changa chili mwa inu Yehova.+Ndipo ndikunena kuti: “Inu ndinu Mulungu wanga.”+ Mateyu 27:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Cha m’ma 3 kolokomo Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” kutanthauza kuti, “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+ Maliko 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo cha m’ma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” Mawu amenewa akawamasulira amatanthauza kuti: “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+
16 Agalu andizungulira.+Khamu la anthu ochita zoipa landizinga.+Iwo akuluma manja ndi mapazi anga ngati mkango.+
14 Koma ine chikhulupiriro changa chili mwa inu Yehova.+Ndipo ndikunena kuti: “Inu ndinu Mulungu wanga.”+
46 Cha m’ma 3 kolokomo Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” kutanthauza kuti, “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+
34 Ndipo cha m’ma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” Mawu amenewa akawamasulira amatanthauza kuti: “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+