Yobu 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mdima wandiweyani ulitenge.Mtambo wa mvula uliphimbe.Zinthu zimene zimadetsa tsiku ziliopseze.+ Yobu 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi anakuvundukulira zipata za imfa,+Kapena zipata za mdima wandiweyani,+ kodi ungathe kuziona? Salimo 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale ndikuyenda m’chigwa cha mdima wandiweyani,+Sindikuopa kanthu,+Pakuti inu muli ndi ine.+Chibonga chanu ndi ndodo yanu ndi zimene zimandilimbikitsa.+ Salimo 88:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi zodabwitsa zimene inu mukuchita zidzadziwika mu mdima?+Kapena kodi chilungamo chanu chidzadziwika m’dziko la anthu oiwalika?+ Mlaliki 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+
4 Ngakhale ndikuyenda m’chigwa cha mdima wandiweyani,+Sindikuopa kanthu,+Pakuti inu muli ndi ine.+Chibonga chanu ndi ndodo yanu ndi zimene zimandilimbikitsa.+
12 Kodi zodabwitsa zimene inu mukuchita zidzadziwika mu mdima?+Kapena kodi chilungamo chanu chidzadziwika m’dziko la anthu oiwalika?+
10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+