Yobu 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mdima wandiweyani ulitenge.* Mtambo wa mvula uliphimbe. Zinthu zimene zimadetsa tsiku ziliopseze.