Yobu 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mdima wandiweyani ulitenge.Mtambo wa mvula uliphimbe.Zinthu zimene zimadetsa tsiku ziliopseze.+