Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 31:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndaiwalidwa ngati munthu wakufa amene anthu sakumukumbukiranso.+

      Ndakhala ngati chiwiya chosweka.+

  • Mlaliki 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti munthu wanzeru, mofanana ndi wopusa, sadzakumbukiridwa mpaka kalekale.+ M’masiku amene akubwerawa aliyense adzaiwalidwa. Ndipo kodi wanzeru adzafa motani? Adzafa mofanana ndi wopusa.+

  • Mlaliki 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma ngakhale zili choncho, ndaona anthu oipa akuikidwa m’manda.+ Ndaonanso mmene iwo anabwerera ndi mmene anachokera pamalo oyera,+ n’kuiwalika mumzinda umene anali kuchitiramo zoipazo.+ Izinso n’zachabechabe.

  • Mlaliki 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena