Mlaliki 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi munthu wanzeru amaposa bwanji munthu wopusa?+ Kodi munthu wovutika amapindula chiyani chifukwa chodziwa mmene angachitire zinthu ndi anthu? Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . . Aheberi 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Monga mmene zilili ndi anthu kuti amayembekezera+ kufa kamodzi kokha, kenako n’kudzalandira chiweruzo,+
8 Kodi munthu wanzeru amaposa bwanji munthu wopusa?+ Kodi munthu wovutika amapindula chiyani chifukwa chodziwa mmene angachitire zinthu ndi anthu?
12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .
27 Monga mmene zilili ndi anthu kuti amayembekezera+ kufa kamodzi kokha, kenako n’kudzalandira chiweruzo,+