Ekisodo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Patapita nthawi, mfumu ina yomwe sinam’dziwe Yosefe inayamba kulamulira mu Iguputo.+ Salimo 103:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mphepo ikawomba limafa,+Ndipo pamalo amene linali sipadziwikanso,+ Mlaliki 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu akale sakumbukiridwa, ndipo amene adzakhalepo m’tsogolo sadzakumbukiridwanso.+ Iwowanso sadzakumbukiridwa ndi amene adzakhalepo m’tsogolo mwawo.+
11 Anthu akale sakumbukiridwa, ndipo amene adzakhalepo m’tsogolo sadzakumbukiridwanso.+ Iwowanso sadzakumbukiridwa ndi amene adzakhalepo m’tsogolo mwawo.+