Yobu 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sadzabwereranso kunyumba yake,Ndipo anthu a pamalo ake sadzamuzindikiranso.+ Yobu 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Diso limene lamuona silidzam’penyanso,+Ndipo malo ake sadzamuonanso.+