Yobu 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Wina akam’meza pamalo ake,+Malowo adzamukana kuti, ‘Sindinakuonepo.’+ Salimo 103:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mphepo ikawomba limafa,+Ndipo pamalo amene linali sipadziwikanso,+