Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 37:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ana ake onse aamuna ndi aakazi anali kupita kukam’tonthoza,+ koma iye anali kukana kutonthozedwa. Anali kunena kuti:+ “Ayi! Ndidzalira mpaka kutsikira ku Manda* kumene kuli mwana wanga.” Ndipo bambo akewo anapitiriza kumulira.

  • 1 Mafumu 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iweyo uchite zinthu monga mwa nzeru zako,+ ndipo usalole kuti imvi zake zitsikire ku Manda*+ mwamtendere.+

  • Yesaya 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho, Manda* akulitsa malo ake ndipo atsegula kwambiri pakamwa pake kupitirira malire.+ Anthu olemekezeka a mumzindawo, khamu lake, phokoso lake ndi chikondwerero chake zidzatsikira m’mandamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena