Miyambo 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mfumu yanzeru imabalalitsa anthu oipa,+ ndipo imawaponda ndi wilo lopunthira.+