Salimo 77:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa tsiku la zowawa zanga ndafunafuna Yehova.+Ndakweza dzanja langa kumwamba usiku wonse, ndipo silinachite dzanzi.Koma sindinatonthozeke.+ Mateyu 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mawu anamveka ku Rama,+ kulira ndi kubuma mofuula. Anali Rakele+ kulirira ana ake ndipo sanamve kumutonthoza, chifukwa ana akewo kunalibenso.”
2 Pa tsiku la zowawa zanga ndafunafuna Yehova.+Ndakweza dzanja langa kumwamba usiku wonse, ndipo silinachite dzanzi.Koma sindinatonthozeke.+
18 “Mawu anamveka ku Rama,+ kulira ndi kubuma mofuula. Anali Rakele+ kulirira ana ake ndipo sanamve kumutonthoza, chifukwa ana akewo kunalibenso.”