Salimo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi magazi anga angakhale ndi phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+Kodi fumbi lidzakutamandani?+ Kodi lidzalengeza kuti inu ndinu woona?+ Salimo 115:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akufa satamanda Ya,+Ngakhalenso aliyense wotsikira kuli chete.+ Yesaya 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti Manda sangakutamandeni.+ Imfa singakulemekezeni.+Anthu amene akutsikira kudzenje sangayembekezere kukhulupirika kwanu.+
9 Kodi magazi anga angakhale ndi phindu lanji ngati nditatsikira kudzenje la manda?+Kodi fumbi lidzakutamandani?+ Kodi lidzalengeza kuti inu ndinu woona?+
18 Pakuti Manda sangakutamandeni.+ Imfa singakulemekezeni.+Anthu amene akutsikira kudzenje sangayembekezere kukhulupirika kwanu.+