Mlaliki 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+ Yesaya 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndanena kuti: “Sindidzamuona Ya.* Ndithu Ya sindidzam’penya m’dziko la amoyo.+Anthu sindidzawaonanso. Ndidzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.
5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+
11 Ndanena kuti: “Sindidzamuona Ya.* Ndithu Ya sindidzam’penya m’dziko la amoyo.+Anthu sindidzawaonanso. Ndidzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.