Salimo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti akufa satchula za inu.+Kodi ndani angatamande inu ali m’Manda?*+ Salimo 115:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akufa satamanda Ya,+Ngakhalenso aliyense wotsikira kuli chete.+ Mlaliki 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+
10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+