Salimo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mawu a pakamwa panga ndi kusinkhasinkha kwa mtima wanga,+Zikukondweretseni, inu Yehova, Thanthwe langa+ ndi Wondiwombola.+ Yesaya 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+
14 Mawu a pakamwa panga ndi kusinkhasinkha kwa mtima wanga,+Zikukondweretseni, inu Yehova, Thanthwe langa+ ndi Wondiwombola.+
17 M’malo mopeza mtendere ndinapeza zowawa, zowawatu zedi!+Inuyo mwamamatira moyo wanga ndipo mwauteteza kuti usapite kudzenje la chiwonongeko.+Pakuti machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.+