Salimo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali?+N’chifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya masautso?+ Salimo 71:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu, musakhale kutali ndi ine.+Inu Mulungu wanga, fulumirani kundithandiza.+
10 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali?+N’chifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya masautso?+