Salimo 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musakhale kutali ndi ine, chifukwa zondisautsa zili pafupi,+Ndiponso chifukwa ndilibe mthandizi winanso.+ Salimo 70:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Inu Mulungu, fulumirani kundilanditsa,+Inu Yehova, fulumirani kundithandiza.+
11 Musakhale kutali ndi ine, chifukwa zondisautsa zili pafupi,+Ndiponso chifukwa ndilibe mthandizi winanso.+