Salimo 72:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti adzalanditsa wosauka amene akufuula popempha thandizo,+Komanso wosautsika ndi aliyense wopanda womuthandiza.+ Luka 23:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Pamenepo Yesu anafuula mokweza mawu kuti: “Atate, ndikuikiza mzimu*+ wanga m’manja mwanu.” Atanena zimenezi anatsirizika.+
12 Pakuti adzalanditsa wosauka amene akufuula popempha thandizo,+Komanso wosautsika ndi aliyense wopanda womuthandiza.+
46 Pamenepo Yesu anafuula mokweza mawu kuti: “Atate, ndikuikiza mzimu*+ wanga m’manja mwanu.” Atanena zimenezi anatsirizika.+