Salimo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+N’chifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?+N’chifukwa chiyani simukumva mawu a kubuula kwanga?+ Yeremiya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu chiyembekezo cha Isiraeli,+ Mpulumutsi wake+ pa nthawi ya nsautso,+ n’chifukwa chiyani mukukhala ngati mlendo m’dzikoli? N’chifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wapaulendo amene wapatuka kuti agone usiku umodzi wokha?+
22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+N’chifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?+N’chifukwa chiyani simukumva mawu a kubuula kwanga?+
8 Inu chiyembekezo cha Isiraeli,+ Mpulumutsi wake+ pa nthawi ya nsautso,+ n’chifukwa chiyani mukukhala ngati mlendo m’dzikoli? N’chifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wapaulendo amene wapatuka kuti agone usiku umodzi wokha?+