Salimo 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu Yehova, mwaona zimenezi+ ndipo musakhale chete.+Musakhale patali ndi ine, inu Yehova.+ Salimo 38:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, musandisiye.Inu Mulungu wanga, musakhale kutali ndi ine.+