Salimo 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musakhale kutali ndi ine, chifukwa zondisautsa zili pafupi,+Ndiponso chifukwa ndilibe mthandizi winanso.+ Salimo 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu Yehova, mwaona zimenezi+ ndipo musakhale chete.+Musakhale patali ndi ine, inu Yehova.+
11 Musakhale kutali ndi ine, chifukwa zondisautsa zili pafupi,+Ndiponso chifukwa ndilibe mthandizi winanso.+