Salimo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi mudzandiiwala kufikira liti, inu Yehova?+ Mpaka muyaya?+Mudzandibisira nkhope yanu kufikira liti?+ Salimo 44:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 N’chifukwa chiyani mukubisabe nkhope yanu?N’chifukwa chiyani mukuiwala masautso athu ndi kuponderezedwa kwathu?+
13 Kodi mudzandiiwala kufikira liti, inu Yehova?+ Mpaka muyaya?+Mudzandibisira nkhope yanu kufikira liti?+
24 N’chifukwa chiyani mukubisabe nkhope yanu?N’chifukwa chiyani mukuiwala masautso athu ndi kuponderezedwa kwathu?+