Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Upange chifanizo cha njoka yapoizoni* ndipo uchiike pamtengo wachizindikiro. Munthu aliyense amene walumidwa, akayang’ana njokayo akhalebe ndi moyo.”+

  • 2 Mafumu 20:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Bwerera, kauze Hezekiya mtsogoleri+ wa anthu anga kuti, ‘Yehova Mulungu+ wa Davide kholo lako wanena kuti: “Ndamva+ pemphero lako,+ ndipo ndaona misozi yako.+ Ndikuchiritsa.+ Pa tsiku lachitatu udzapita kunyumba ya Yehova.+

  • Salimo 30:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Inu Yehova Mulungu wanga, ndinafuulira kwa inu kuti mundithandize ndipo munandichiritsa.+

  • Salimo 103:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Tamanda amene akukukhululukira zolakwa zako zonse,+

      Iye amene akukuchiritsa matenda ako onse.+

  • Salimo 147:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye amachiritsa+ anthu osweka mtima,+

      Ndipo amamanga zilonda zawo zopweteka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena