Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndiyeno anawauza kuti: “Ngati mudzamveradi mawu a Yehova Mulungu wanu, ndi kuchita zinthu zoyenera pamaso pake ndiponso kumvera malamulo ake ndi kusunga malangizo ake onse,+ sindidzakugwetserani miliri iliyonse imene ndinagwetsera Iguputo,+ chifukwa ine ndine Yehova amene ndikukuchiritsani.”+

  • Deuteronomo 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova adzakuchotserani matenda onse. Ndipo sadzakugwetserani matenda onse oipa a ku Iguputo amene inu mukuwadziwa,+ koma adzawagwetsera pa onse odana nanu.

  • Salimo 41:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Yehova adzachirikiza wonyozekayo pamene akudwala pabedi lake.+

      Mudzamusamalira bwino kwambiri pamene akudwala.+

  • Salimo 147:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye amachiritsa+ anthu osweka mtima,+

      Ndipo amamanga zilonda zawo zopweteka.+

  • Yesaya 33:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Palibe munthu wokhala m’dzikolo amene adzanene kuti: “Ndikudwala.”+ Anthu okhala mmenemo adzakhala amene machimo awo anakhululukidwa.+

  • Yeremiya 17:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndichiritseni inu Yehova, ndipo ndidzachiradi.+ Ndipulumutseni ndipo ndidzapulumukadi,+ pakuti ine ndimatamanda inu.+

  • Yakobo 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pemphero lachikhulupiriro lidzachiritsa wodwalayo,+ ndipo Yehova adzamulimbitsa.+ Ndiponso ngati anachita machimo, adzakhululukidwa.+

  • Chivumbulutso 21:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iye adzapukuta misozi+ yonse m’maso mwawo, ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira,+ kapena kubuula, ngakhale kupweteka. Zakalezo zapita.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena