Ekisodo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho iwo anatenga mwaye wa mu uvuni ndi kuima pamaso pa Farao. Pamenepo Mose anauponya m’mwamba, ndipo unayambitsa zithupsa zomaphulika,+ pa anthu ndi nyama. Deuteronomo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova adzakuchotserani matenda onse. Ndipo sadzakugwetserani matenda onse oipa a ku Iguputo amene inu mukuwadziwa,+ koma adzawagwetsera pa onse odana nanu.
10 Choncho iwo anatenga mwaye wa mu uvuni ndi kuima pamaso pa Farao. Pamenepo Mose anauponya m’mwamba, ndipo unayambitsa zithupsa zomaphulika,+ pa anthu ndi nyama.
15 Yehova adzakuchotserani matenda onse. Ndipo sadzakugwetserani matenda onse oipa a ku Iguputo amene inu mukuwadziwa,+ koma adzawagwetsera pa onse odana nanu.