Ekisodo 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Muzitumikira Yehova Mulungu wanu,+ ndipo adzakudalitsani ndi chakudya ndi madzi.+ Ndipo ndidzachotsa matenda pakati panu.+ Salimo 103:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamanda amene akukukhululukira zolakwa zako zonse,+Iye amene akukuchiritsa matenda ako onse.+
25 Muzitumikira Yehova Mulungu wanu,+ ndipo adzakudalitsani ndi chakudya ndi madzi.+ Ndipo ndidzachotsa matenda pakati panu.+