Afilipi 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Inde, n’zoona, anadwaladi kutsala pang’ono kufa. Koma Mulungu anam’chitira chifundo.+ Ndipo chifundo chimenecho sanachitire iye yekha ayi, koma inenso, kuti chisoni changa chisawonjezeke.
27 Inde, n’zoona, anadwaladi kutsala pang’ono kufa. Koma Mulungu anam’chitira chifundo.+ Ndipo chifundo chimenecho sanachitire iye yekha ayi, koma inenso, kuti chisoni changa chisawonjezeke.