Salimo 66:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzalowa m’nyumba yanu ndi nsembe zopsereza zathunthu.+Ine ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa inu+ Salimo 116:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa Yehova,+Pamaso pa anthu ake onse. Salimo 121:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 121 Ndakweza maso anga kuyang’ana kumapiri.+Kodi thandizo langa lichokera kuti?+
13 Ndidzalowa m’nyumba yanu ndi nsembe zopsereza zathunthu.+Ine ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa inu+ Salimo 116:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa Yehova,+Pamaso pa anthu ake onse. Salimo 121:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 121 Ndakweza maso anga kuyang’ana kumapiri.+Kodi thandizo langa lichokera kuti?+