Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Nkhope yanga yafiira chifukwa cholira,+

      Ndipo pazikope zanga pali mdima wandiweyani,+

  • Salimo 39:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,

      Ndipo tcherani khutu pamene ndikufuula kupempha thandizo.+

      Musandinyalanyaze pamene ndikugwetsa misozi.+

      Pakuti ndine mlendo wanu,+

      Mlendo wokhala nanu monga anachitira makolo anga onse.+

  • Salimo 126:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Amene akukhetsa misozi pofesa mbewu,+

      Adzakolola akufuula mosangalala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena