Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 25:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “‘Choncho musamagulitsiretu malo anu mpaka kalekale+ chifukwa dzikolo ndi langa.+ Kwa ine, inu ndinu alendo m’dziko langa.+

  • 1 Mbiri 29:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala m’dziko la eni+ monga analili makolo athu onse. Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi,+ ndipo ndife osakhalitsa.

  • Salimo 119:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  19 Ine ndine mlendo m’dziko ili.+

      Musandibisire malamulo anu.+

  • 1 Petulo 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiponso, ngati mukupempha zinthu kwa Atate, amene amaweruza mopanda tsankho+ malinga ndi ntchito za aliyense, chitani zinthu ndi mantha+ pa nthawi imene muli ngati alendo m’dzikoli.+

  • 1 Petulo 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa m’dzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa zilakolako za thupi+ zimene zili pa nkhondo yolimbana ndi moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena