1 Mafumu 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Naboti anayankha Ahabu kuti: “Sindingachite zimenezo+ pamaso pa Yehova,+ kupereka cholowa cha makolo anga kwa inuyo.”+ Ezekieli 48:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aleviwo asagulitse mbali iliyonse ya malowo kapena kuwasinthanitsa ndi chilichonse. Aliyense asapereke malo abwino kwambiriwo kwa munthu wa fuko lina pakuti ndi malo opatulika kwa Yehova.+
3 Koma Naboti anayankha Ahabu kuti: “Sindingachite zimenezo+ pamaso pa Yehova,+ kupereka cholowa cha makolo anga kwa inuyo.”+
14 Aleviwo asagulitse mbali iliyonse ya malowo kapena kuwasinthanitsa ndi chilichonse. Aliyense asapereke malo abwino kwambiriwo kwa munthu wa fuko lina pakuti ndi malo opatulika kwa Yehova.+