Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma mukaonetsetse kuti mukusunga malamulo+ ndi Chilamulo chimene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani. Mukachite zimenezi mwa kukonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda m’njira zake zonse,+ kusunga malamulo ake,+ kum’mamatira,+ ndiponso kum’tumikira+ ndi mtima wanu wonse+ ndiponso moyo wanu wonse.”+

  • 1 Samueli 24:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho iye anauza amuna amene anali kuyenda naye kuti: “Sindinayenere m’pang’ono pomwe kuchitira mbuyanga zimenezi pamaso pa Yehova. Iye ndi wodzozedwa+ wa Yehova. Sindinayenere kutambasula dzanja langa ndi kumuukira, pakuti iye ndi wodzozedwa wa Yehova.”+

  • 1 Samueli 26:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kwa ine, n’zosatheka!+ Sindingachite zimenezi pamaso pa Yehova.+ Sindingatambasule dzanja langa+ ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+ Choncho, tiye titenge mkondo umene uli chakumutu kwakewo, ndi mtsuko wa madziwo tizipita.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena