Ekisodo 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Usatemberere Mulungu+ kapena kutemberera mtsogoleri amene ali pakati pa anthu ako.+ 1 Mbiri 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anati: ‘Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.’+ Salimo 105:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+ Machitidwe 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Paulo anati: “Abale, sindinadziwe kuti ndi mkulu wa ansembe. Pakuti Malemba amati, ‘Wolamulira wa anthu a mtundu wako usamunenere zachipongwe.’”+
22 Iye anati: ‘Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.’+
15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+
5 Pamenepo Paulo anati: “Abale, sindinadziwe kuti ndi mkulu wa ansembe. Pakuti Malemba amati, ‘Wolamulira wa anthu a mtundu wako usamunenere zachipongwe.’”+