Genesis 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano bweza mkaziyo kwa mwamuna wake. Mwamunayo ndi mneneri,+ ndipo adzakupempherera.+ Ukatero udzakhala ndi moyo. Koma ukapanda kumubweza, udziwe kuti, iweyo ndi anthu ako onse mufa ndithu.”+ Salimo 105:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+
7 Tsopano bweza mkaziyo kwa mwamuna wake. Mwamunayo ndi mneneri,+ ndipo adzakupempherera.+ Ukatero udzakhala ndi moyo. Koma ukapanda kumubweza, udziwe kuti, iweyo ndi anthu ako onse mufa ndithu.”+
15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+