Deuteronomo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mose anaitana Aisiraeli+ onse n’kuwauza kuti: “Inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo+ zimene ndikukuuzani lero, ndipo muziphunzire ndi kuzitsatira mosamala.+ Deuteronomo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo mawu awa amene ndikukulamula lero azikhala pamtima pako,+ Deuteronomo 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Muzichita mosamala mawu onse amene ndikukuuzani.+ Musawonjezepo kapena kuchotsapo kalikonse.+ 2 Mafumu 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sindidzachititsanso phazi la Isiraeli kuchoka panthaka imene ndinapatsa makolo awo,+ ngati atayesetsa kuchita zinthu mogwirizana ndi zonse zimene ndinawalamula,+ ndiponso mogwirizana ndi chilamulo chonse chimene Mose mtumiki wanga anawalamula.”
5 Ndiyeno Mose anaitana Aisiraeli+ onse n’kuwauza kuti: “Inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo+ zimene ndikukuuzani lero, ndipo muziphunzire ndi kuzitsatira mosamala.+
8 Sindidzachititsanso phazi la Isiraeli kuchoka panthaka imene ndinapatsa makolo awo,+ ngati atayesetsa kuchita zinthu mogwirizana ndi zonse zimene ndinawalamula,+ ndiponso mogwirizana ndi chilamulo chonse chimene Mose mtumiki wanga anawalamula.”