Deuteronomo 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Mukasungadi malamulo onsewa+ amene ndikukupatsani, kukonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda m’njira zake zonse+ ndi kum’mamatira,+ Deuteronomo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake, muzim’tumikira ndi kum’mamatira.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
22 “Mukasungadi malamulo onsewa+ amene ndikukupatsani, kukonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda m’njira zake zonse+ ndi kum’mamatira,+
4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake, muzim’tumikira ndi kum’mamatira.+
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+