Deuteronomo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzionetsetsa kuti mukusunga malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ maumboni ake+ ndi zigamulo+ zake zimene wakupatsani.+ Deuteronomo 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndiyeno mukadzamveradi malamulo anga+ amene ndikukupatsani lero, moti n’kukonda Yehova Mulungu wanu ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+ Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.
17 Muzionetsetsa kuti mukusunga malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ maumboni ake+ ndi zigamulo+ zake zimene wakupatsani.+
13 “Ndiyeno mukadzamveradi malamulo anga+ amene ndikukupatsani lero, moti n’kukonda Yehova Mulungu wanu ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.