Deuteronomo 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Mukasungadi malamulo onsewa+ amene ndikukupatsani, kukonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda m’njira zake zonse+ ndi kum’mamatira,+ Salimo 119:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mwatilamula kuti tisunge+Malamulo anu mosamala.+
22 “Mukasungadi malamulo onsewa+ amene ndikukupatsani, kukonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda m’njira zake zonse+ ndi kum’mamatira,+