Deuteronomo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse,+ moyo wako wonse,+ ndi mphamvu zako zonse.+ Luka 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anayankha kuti: “‘Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, mphamvu zako zonse, ndi maganizo ako onse.’+ Komanso, ‘uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’”+
27 Iye anayankha kuti: “‘Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, mphamvu zako zonse, ndi maganizo ako onse.’+ Komanso, ‘uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’”+