Deuteronomo 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+ Deuteronomo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse,+ moyo wako wonse,+ ndi mphamvu zako zonse.+ Deuteronomo 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndiyeno mukadzamveradi malamulo anga+ amene ndikukupatsani lero, moti n’kukonda Yehova Mulungu wanu ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+ Maliko 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, maganizo ako onse ndi mphamvu zako zonse.’+
29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+
13 “Ndiyeno mukadzamveradi malamulo anga+ amene ndikukupatsani lero, moti n’kukonda Yehova Mulungu wanu ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+
30 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, maganizo ako onse ndi mphamvu zako zonse.’+