-
1 Samueli 14:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Koma anthu anauza Sauli kuti: “Kodi Yonatani amene wagwira ntchito yobweretsa chipulumutso chachikulu chimenechi+ mu Isiraeli afe? Sizitheka zimenezo!+ Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ ngakhale tsitsi limodzi+ la m’mutu wake siligwa pansi, pakuti iye wachita zimenezi lero mothandizidwa ndi Mulungu.”+ Ndi mawu amenewa anthuwo anapulumutsa+ Yonatani, moti sanafe.
-