1 Samueli 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kwa ine, n’zosatheka!+ Sindingachite zimenezi pamaso pa Yehova.+ Sindingatambasule dzanja langa+ ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+ Choncho, tiye titenge mkondo umene uli chakumutu kwakewo, ndi mtsuko wa madziwo tizipita.” 2 Samueli 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Davide anati: “Zinatheka bwanji iwe osaopa+ kutambasula dzanja lako ndi kukantha wodzozedwa+ wa Yehova?”
11 Kwa ine, n’zosatheka!+ Sindingachite zimenezi pamaso pa Yehova.+ Sindingatambasule dzanja langa+ ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+ Choncho, tiye titenge mkondo umene uli chakumutu kwakewo, ndi mtsuko wa madziwo tizipita.”
14 Pamenepo Davide anati: “Zinatheka bwanji iwe osaopa+ kutambasula dzanja lako ndi kukantha wodzozedwa+ wa Yehova?”