1 Mafumu 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Solomo atamva anati: “Akadzakhala munthu wolimba mtima, ngakhale tsitsi lake limodzi+ silidzathothoka n’kugwera pansi, koma choipa chikadzapezeka mwa iye,+ adzaphedwa.”+ Luka 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komatu ngakhale tsitsi limodzi lokha+ la m’mutu mwanu silidzawonongeka ayi. Machitidwe 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho ndikukulimbikitsani kuti mudye kuti zinthu zikuyendereni bwino. Pakuti ngakhale tsitsi+ limodzi la kumutu kwa aliyense wa inu siliwonongeka.”
52 Solomo atamva anati: “Akadzakhala munthu wolimba mtima, ngakhale tsitsi lake limodzi+ silidzathothoka n’kugwera pansi, koma choipa chikadzapezeka mwa iye,+ adzaphedwa.”+
34 Choncho ndikukulimbikitsani kuti mudye kuti zinthu zikuyendereni bwino. Pakuti ngakhale tsitsi+ limodzi la kumutu kwa aliyense wa inu siliwonongeka.”