Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 14:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Koma anthu anauza Sauli kuti: “Kodi Yonatani amene wagwira ntchito yobweretsa chipulumutso chachikulu chimenechi+ mu Isiraeli afe? Sizitheka zimenezo!+ Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ ngakhale tsitsi limodzi+ la m’mutu wake siligwa pansi, pakuti iye wachita zimenezi lero mothandizidwa ndi Mulungu.”+ Ndi mawu amenewa anthuwo anapulumutsa+ Yonatani, moti sanafe.

  • 2 Samueli 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma mkaziyo anati: “Chonde mfumu, kumbukirani Yehova Mulungu wanu+ kuti munthu wobwezera magazi+ asapitirize kuwononga, ndi kuti anthu amenewa asaphe mwana wanga.” Pamenepo mfumu inati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ ngakhale tsitsi limodzi+ la mwana wako silidzagwa pansi.”

  • Mateyu 10:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndipotu tsitsi lenilenilo la m’mutu mwanu amaliwerenga.+

  • Luka 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndipo ngakhale tsitsi+ lonse la m’mutu mwanu analiwerenga. Musachite mantha. Ndinu ofunika kwambiri kuposa mpheta zambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena