Deuteronomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uziopa Yehova Mulungu wako+ ndi kum’tumikira,+ ndipo uzilumbira pa dzina lake.+ 1 Samueli 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi yomweyo, Sauli anamulumbirira m’dzina la Yehova kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ sukhala ndi mlandu chifukwa cha nkhani imeneyi!” Mlaliki 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa mawu a mfumu ali ndi mphamvu yolamulira,+ ndipo ndani angaifunse kuti: ‘Kodi mukuchita chiyani?’”
10 Nthawi yomweyo, Sauli anamulumbirira m’dzina la Yehova kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ sukhala ndi mlandu chifukwa cha nkhani imeneyi!”
4 chifukwa mawu a mfumu ali ndi mphamvu yolamulira,+ ndipo ndani angaifunse kuti: ‘Kodi mukuchita chiyani?’”