Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 14:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndithu, pali Yehova Mulungu wamoyo, Mlanditsi wa Isiraeli, munthu amene wachititsa tchimoli ayenera kufa ndithu,+ ngakhale atakhala Yonatani mwana wanga.” Koma panalibe ngakhale munthu mmodzi womuyankha mwa anthu onsewo.

  • Yesaya 48:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Mverani izi inu a m’nyumba ya Yakobo, inu amene mumadzitcha ndi dzina la Isiraeli,+ amene munatuluka kuchokera m’madzi a Yuda,+ amene mumalumbira pa dzina la Yehova,+ ndiponso inu amene mumaitana Mulungu wa Isiraeli,+ koma osati m’choonadi kapena m’chilungamo.+

  • Yeremiya 44:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Tsopano imvani mawu a Yehova, inu nonse a ku Yuda amene mukukhala mu Iguputo muno.+ Yehova wanena kuti: “Ine ndalumbira m’dzina langa+ kuti m’dziko lonse la Iguputo simudzapezeka munthu aliyense wa ku Yuda woitanira pa dzina langa+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Ambuye Wamkulu Koposa!’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena