Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma Sauli anayankha kuti: “Lero pasaphedwe munthu aliyense,+ chifukwa Yehova watipulumutsa mu Isiraeli.”+

  • 1 Samueli 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Nthawi yoyamba imene Yonatani ndi mtumiki wakeyo anakantha Afilisitiwo anapha anthu 20, pamalo okwana pafupifupi hafu ya m’litali mwa ekala.*

  • 1 Samueli 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iye anaika moyo wake pangozi*+ n’kupha Mfilisiti uja,+ moti Yehova anapereka chipulumutso chachikulu+ kwa Aisiraeli onse. Inuyo munaona zimenezi zikuchitika, ndipo munasangalala. Ndiye n’chifukwa chiyani mukufuna kuchimwira magazi osalakwa, mwa kupha Davide+ popanda chifukwa?”+

  • Nehemiya 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chifukwa chochita zimenezi, munawapereka m’manja mwa adani awo+ amene anapitiriza kuwasautsa.+ Koma akakumana ndi nsautso, anali kukulirirani,+ ndipo inu munali kumva muli kumwambako.+ Chifukwa cha chifundo chanu chachikulu,+ munali kuwapatsa owapulumutsa+ amene anali kuwalanditsa m’manja mwa adani awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena